1 Mafumu 13:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa iye, Inenso ndine mneneri wonga iwe, ndipo mthenga analankhula ndi ine mwa mau a Yehova, nati, Kambwezere kwanu, kuti akadye mkate, namwe madzi. Koma anamnamiza.

1 Mafumu 13

1 Mafumu 13:11-20