1 Mafumu 13:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Natsata munthu wa Mulungu, nampeza ali, tsonga patsinde pa mtengo wathundu, nanena naye, Kodi ndiwe munthu wa Mulungu amene uja anacokera ku Yuda? Nati, Ndine amene.

1 Mafumu 13

1 Mafumu 13:10-16