1 Mafumu 13:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onani, munthu wa Mulungu anacokera ku Yuda mwa mau a Yehova nadza ku Beteli; ndipo Yerobiamu anali kuimirira m'mbali mwa guwa la nsembe kufukiza zonunkhira.

1 Mafumu 13

1 Mafumu 13:1-7