1 Mafumu 12:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anamuuza kuti, Mukakhala inu mtumiki wa anthu awa lero, ndi kuwatumikira ndi kuwayankha ndi kukamba nao mau okoma, tsono iwo adzakhala cikhalire atumiki anu.

1 Mafumu 12

1 Mafumu 12:6-8