1 Mafumu 12:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali kuti Yerobiamu mwana wa Nebati anacimva akali m'Aigupto, kumene anathawira kucokera ku maso a Solomo mfumu, pakuti Yerobiamu anakhala ku Aigupto.

1 Mafumu 12

1 Mafumu 12:1-9