1 Mafumu 11:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, atakalamba Solomo, akazi ace anapambutsa mtima wace atsate milungu yina; ndipo mtima wace sunakhala wangwiro ndi Yehova Mulungu wace monga mtima wa Davide atate wace.

1 Mafumu 11

1 Mafumu 11:2-5