1 Mafumu 11:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati kwa Yerobiamu, Takwaya magawo khumi; popeza atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Taona ndidzaung'amba ufumu m'dzanja la Solomo ndi kukupatsa iwe mafuko khumi.

1 Mafumu 11

1 Mafumu 11:26-41