1 Mafumu 11:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono Farao anati kwa iye, Koma cikusowa iwe nciani kwa ine, kuti ufuna kumuka ku dziko la kwanu? Nayankha iye, Palibe kanthu, koma mundilole ndimuke ndithu.

1 Mafumu 11

1 Mafumu 11:20-23