1 Mafumu 11:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacoka ku Midyani nafika ku Parani, natenga anthu a ku Parani pamodzi nao, nafika ku Aigupto kwa Farao mfumu ya Aigupto, ameneyo anampatsa nyumba, namnenera zakudya, nampatsako dziko.

1 Mafumu 11

1 Mafumu 11:11-19