1 Mafumu 10:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mpandowo wacifumu unali ndi makwerero asanu ndi limodzi, ndi pamwamba pa mpando wacifumu panali pozungulira kumbuyoko, ndipo munali ngati manja m'mbali zonse ziwiri za pokhalirapo, naimika mikango iwiri m'mbali mwa manjawo.

1 Mafumu 10

1 Mafumu 10:10-26