1 Mafumu 10:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono kulemera kwace kwa golidi anafika kwa Solomo caka cimodzi kunali matalenti mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi kudza asanu ndi liimodzi a golidi,

1 Mafumu 10

1 Mafumu 10:4-18