1 Mafumu 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Adoniya mwana wa Hagiti anadzikuza, nati, Ndikhala mfumu ndine; nadzikonzera agareta ndi apakavalo ndi anthu makumi asanu omtsogolera mothamanga.

1 Mafumu 1

1 Mafumu 1:1-8