1 Mafumu 1:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Zadoki wansembe anatenga nyanga ya mafuta inali m'Cihema, namdzoza Solomo. Ndipo iwo anaomba lipenga, ndi anthu onse anati, Mfumu Solomo akhale ndi moyo.

1 Mafumu 1

1 Mafumu 1:35-49