1 Mafumu 1:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anyamata ace ananena naye, Amfunire mbuye wanga mfumu namwali, aimirire pamaso pa mfumu namsunge; nagone m'mfukato mwanu, kuti mbuye mfumu yanga afundidwe.

1 Mafumu 1

1 Mafumu 1:1-8