1 Atesalonika 5:27-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Ndikulumbirirani pa Ambuye kuti 2 kalatayu awerengedwe kwa abale onse.

28. Cisomo ca Ambuye wathu Yesu Kristu cikhale nanu.

1 Atesalonika 5