1 Atesalonika 5:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma za nthawizo ndi nyengozo, abale, sikufunika kuti tidzakulemberani,

2. Pakuti inu nokha mudziwa bwino kuti tsiku la Ambuye lidzadza monga mbala usiku,

1 Atesalonika 5