1 Atesalonika 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsopano pofika Timoteo kwathu kucokera kwa inu, ndi kutifotokozera mbiri yokoma ya cikhulupiriro ndi cikondano canu, ndi kuti mutikumbukila bwino masiku onse, pokhumba kutiona ife, monganso ire kukuonani inu;

1 Atesalonika 3

1 Atesalonika 3:1-11