1 Atesalonika 2:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti sitinayenda nao mau osyasyalika nthawi iri yonse, monga mudziwa, kapena kupsiniira msiriro, mboni ndi Mulungu;

1 Atesalonika 2

1 Atesalonika 2:1-10