1 Akorinto 9:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngati ena ali nao ulamuliro umene pa inu, si ife nanga koposa? Koma sitinacita nao ulamuliro umene; koma timalola zonse, kuti tingacite cocedwetsa kwa Uthenga Wabwino wa Kristu,

1 Akorinto 9

1 Akorinto 9:10-20