1 Akorinto 9:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kapena acinena ici konse konse cifukwa ca ife? Pakuti, cifukwa ca ife kwalembedwa: popeza wolima ayenera kulima mwa ciyembekezo, ndi wopunthayo acita mwa ciyembekezo ca kugawana nao.

1 Akorinto 9

1 Akorinto 9:1-17