1 Akorinto 8:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti wina akaona iwe amene uli naco cidziwitso, ulikukhala pacakudya m'kacisi wa fano, kodi cikumbu mtima cace, popeza ali wofoka, sieidzalimbika kudya zoperekedwa nsembe kwa mafano?

1 Akorinto 8

1 Akorinto 8:1-12