1 Akorinto 7:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musakanizana, koma ndi kubvomerezana kwanu ndiko, kwa nthawi, kuti mukadzipereke kwa kupemphera, nimukakhalenso pamodzi, kuti Satana angakuyeseni, cifukwa ca kusadziletsa kwanu.

1 Akorinto 7

1 Akorinto 7:2-12