1 Akorinto 6:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kapena simudziwa kuti thupi lanu liri kacisi wa Mzimu Woyera, amene ali mwa inu, amene muli naye kwa Mulungu? Ndipo simukhala a inu nokha.

1 Akorinto 6

1 Akorinto 6:10-20