11. koma tsopano ndalembera inu kuti musayanjane naye, ngati wina wochedwa mbale ali wacigololo, kapena wosirira, kapena wopembedza mafano, kapena wolalatira, kapena woledzera, kapena wolanda, kungakhale kukadya naye wotere, iai.
12. Pakuti nditani nao akunja kukaweruza iwo? Kodi amene ali m'katimosimuwaweruza ndi inu,
13. komaakunia awaweruza Mulungu? Cotsani woipayo pakati pa inu nokha.