1 Akorinto 4:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti akusiyanitsa iwe ndani? Ndipo uli naco ciani cosati wacilandira? Koma ngati wacilandira udzitamanda bwanji, monga ngati sunacilandira?

1 Akorinto 4

1 Akorinto 4:2-8