19. Pakuti nzeru ya dziko ina lapansi iri yopusa kwa Mulungu, Pakuti, kwalembedwa, iye agwira mzeru m'cenjerero lao;
20. ndiponso Ambuye azindikira zolingirira za mzeru, kuti ziri zopanda pace.
21. Cifukwa cace palibemmodzi adziamande mwa anthu. Pakuti zinthu onse nzanu;