1 Akorinto 3:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngati wina aononga kacisi wa Mulungu, ameneyo Mulungu adzamuononga; pakuti kacisi wa Mulungu ali wopatulika, ameneyo ndi inu.

1 Akorinto 3

1 Akorinto 3:11-21