1 Akorinto 16:4-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Ndipo ngati kuyenera kwa ine kupitanso, adzapita nane.

5. Koma ndidzadza kwa inu, nditapyola Makedoniya; pakuti ndidzapyola Makedoniya;

6. ndipo kapena ndidzakhalitsa ndi inu, kapenanso kugonera nyengo yacisanu kuti mukandiperekeze ine kumene kuli konse ndipitako,

7. Pakuti sindifuna kukuonani tsopano popitirira; pakuti ndiyembekeza kukhala ndi inu nthawi, ngati alola Ambuye.

1 Akorinto 16