1 Akorinto 15:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuli ulemerero wa dzuwa, ndi ulemerero wina wa mwezi, ndi ulemerero wina wa nyenyezi; pakuti nyenyezi isiyana ndi nyenyezi m'ulemerero.

1 Akorinto 15

1 Akorinto 15:40-44