1 Akorinto 15:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Ngati ine tsono, kapena iwowa, kotero tilalikira, ndi kotero munakhulupira.

12. Koma ngati Kristu alalikidwa kuti waukitsidwa kwa akufa, nanga ena mwa inu anena bwanjikuti kulibe kuuka kwa akufa?

13. Koma ngati kulibe kuuka kwa akufa, Kristunso sanaukitsidwa;

1 Akorinto 15