1 Akorinto 14:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsopano, abale, ngati ndidza kwa inu ndi kulankhula malilime, ndikaku, pindulitsani ciani, ngati sindilankhui landi inu kapena m'bvumbulutso, kapena m'cidziwitso, kapena m'cinenero, kapena m'ciphunzitsot

1 Akorinto 14

1 Akorinto 14:1-12