1 Akorinto 13:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndingakhale ndikhoza kunenera, ndipo ndingadziwe zinsinsi zonse, ndi nzeru zonse, ndipo ndingakhale ndiri naco cikhulupiriro conse, kuti ndikasendeza mapiri, koma ndiribe cikondi, ndiri cabe.

1 Akorinto 13

1 Akorinto 13:1-11