1 Akorinto 12:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ndikuuzani inu, kuti palibe munthu wakulankhula mwa Mzimu wa Mulungu, anena, Yesu ngwotembereredwa; ndipo palibe wina akhoza kunena, Yew ali Ambuye, koma mwa Mzimu Woyera.

1 Akorinto 12

1 Akorinto 12:1-6