1 Akorinto 12:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma zokoma zathu ziribe kusowa; koma Mulungu analumikizitsa thupi, napatsa ulemu wocuruka kwa cosowaco; kuti kusakhale cisiyano m'thupi;

1 Akorinto 12

1 Akorinto 12:16-31