1 Akorinto 10:31-33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

31. Cifukwa cace 2 mungakhale mudya, mungakhale mumwa, mungakhale mucita kanthu kena, citani zonse ku ulemerero wa Mulungu.

32. 3 Khalani osakhumudwitsa, kapena Ayuda, kapena Ahelene, kapena Mpingo wa Mulungu;

33. monga 4 inenso ndikodweretsa onse m'zinthu zonse, wosafuna cipindulo canga, koma ca unyinjiwo, kuti apulumutsidwe.

1 Akorinto 10