1 Akorinto 10:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sicinakugwerani inu ciyeso koma ca umunthu; koma Mulungu ali wokhulupirika, amene sadzalola inu kuyesedwa koposa kumene mukhoza; koma pamodzi ndi ciyeso adzaikanso populumukirapo, kuti mudzakhoze kupirirako.

1 Akorinto 10

1 Akorinto 10:3-22