1 Akorinto 10:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma izi zinacitika kwa iwowa monga zoticenjeza, ndipo zinalembedwa kuticenjeza ife, amene matsirizidwe a nthawi ya pansi pano adafika pa ife.

1 Akorinto 10

1 Akorinto 10:4-14