1 Akorinto 1:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti popeza m'nzeru ya Mulungu dziko lapansi, mwa nzeru yace, silinadziwa Mulungu, cidamkonda Mulungu kupulumutsa okhulupirawo mwa copusa ca kulalikira.

1 Akorinto 1

1 Akorinto 1:13-22